Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritsidwe mawu onenedwa kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”+

  • Luka 18:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Iwo anamuuza kuti: “Yesu Mnazareti akudutsa!”+

  • Yohane 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pilato analembanso dzina laudindo ndi kuliika pamtengo wozunzikirapowo. Analemba kuti: “Yesu Mnazareti, Mfumu ya Ayuda.”+

  • Machitidwe 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Amuna inu a mu Isiraeli, imvani mawu awa: Yesu Mnazareti,+ ndi munthu amene Mulungu anamuonetsera poyera kwa inu. Anatero mwa ntchito zamphamvu,+ mwa zodabwitsa komanso mwa zizindikiro, zimene Mulungu anachita pakati panu kudzera mwa iye,+ monga mmene inunso mukudziwira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena