Maliko 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Yesu anadzudzula mzimuwo kuti: “Khala chete, ndipo tuluka mwa iye!”+ Maliko 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iye anali kuilamula mwamphamvu nthawi ndi nthawi kuti isamuulule.+ Machitidwe 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtsikana ameneyu anali kumangotsatira Paulo ndi ife n’kumafuula kuti:+ “Anthu awa ndi akapolo a Mulungu Wam’mwambamwamba, ndipo akulengeza njira ya chipulumutso kwa inu.” Machitidwe 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anakhala akuchita zimenezi kwa masiku ambiri. Potsirizira pake Paulo anatopa nazo+ ndipo anatembenuka n’kuuza mzimuwo kuti: “Ndikukulamula m’dzina la Yesu Khristu kuti utuluke mwa mtsikanayu.”+ Nthawi yomweyo mzimuwo unatuluka.+
17 Mtsikana ameneyu anali kumangotsatira Paulo ndi ife n’kumafuula kuti:+ “Anthu awa ndi akapolo a Mulungu Wam’mwambamwamba, ndipo akulengeza njira ya chipulumutso kwa inu.”
18 Iye anakhala akuchita zimenezi kwa masiku ambiri. Potsirizira pake Paulo anatopa nazo+ ndipo anatembenuka n’kuuza mzimuwo kuti: “Ndikukulamula m’dzina la Yesu Khristu kuti utuluke mwa mtsikanayu.”+ Nthawi yomweyo mzimuwo unatuluka.+