Genesis 35:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+ Yeremiya 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkazi amene wabereka ana 7 wafooka ndipo akupuma movutikira.+ Kwa iye dzuwa lalowa masanasana,+ ndipo lachita manyazi ndi kuthedwa nzeru. Anthu otsala ndidzawapereka kwa adani awo kuti aphedwe ndi lupanga,’+ watero Yehova.”
18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+
9 Mkazi amene wabereka ana 7 wafooka ndipo akupuma movutikira.+ Kwa iye dzuwa lalowa masanasana,+ ndipo lachita manyazi ndi kuthedwa nzeru. Anthu otsala ndidzawapereka kwa adani awo kuti aphedwe ndi lupanga,’+ watero Yehova.”