1 Mafumu 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ahabu mwana wa Omuri anakhala mfumu ya Isiraeli m’chaka cha 38 cha Asa mfumu ya Yuda. Iye analamulira Isiraeli ku Samariya+ zaka 22. 1 Mafumu 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.
29 Ahabu mwana wa Omuri anakhala mfumu ya Isiraeli m’chaka cha 38 cha Asa mfumu ya Yuda. Iye analamulira Isiraeli ku Samariya+ zaka 22.
25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.