1 Mafumu 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako anagula phiri la Samariya* kwa Semeri ndi matalente* awiri a siliva. Ndiyeno anayamba kumanga mzinda paphiripo n’kuutcha dzina la Semeri mbuye wa phirilo, loti Samariya.+ 1 Mafumu 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Beni-hadadi anatumizira Ahabu uthenga wakuti: “Milungu+ yanga indilange mowirikiza,+ ngati fumbi la ku Samariya lidzakwanire kuti anthu onse onditsatira atape lodzaza manja.”+ Yesaya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mutu wa Efuraimu ndiwo Samariya,+ ndipo mutu wa Samariya ndiwo mwana wa Remaliya.+ Anthu inu mukakhala opanda chikhulupiriro, simukhalitsa.”’”+
24 Kenako anagula phiri la Samariya* kwa Semeri ndi matalente* awiri a siliva. Ndiyeno anayamba kumanga mzinda paphiripo n’kuutcha dzina la Semeri mbuye wa phirilo, loti Samariya.+
10 Tsopano Beni-hadadi anatumizira Ahabu uthenga wakuti: “Milungu+ yanga indilange mowirikiza,+ ngati fumbi la ku Samariya lidzakwanire kuti anthu onse onditsatira atape lodzaza manja.”+
9 Mutu wa Efuraimu ndiwo Samariya,+ ndipo mutu wa Samariya ndiwo mwana wa Remaliya.+ Anthu inu mukakhala opanda chikhulupiriro, simukhalitsa.”’”+