1 Mafumu 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako aliyense anayamba kupha mdani wake. Asiriyawo+ anayamba kuthawa+ ndipo Aisiraeli anawathamangitsa. Koma Beni-hadadi mfumu ya Siriya anathawa atakwera hatchi, pamodzi ndi amuna ena okwera pamahatchi.
20 Kenako aliyense anayamba kupha mdani wake. Asiriyawo+ anayamba kuthawa+ ndipo Aisiraeli anawathamangitsa. Koma Beni-hadadi mfumu ya Siriya anathawa atakwera hatchi, pamodzi ndi amuna ena okwera pamahatchi.