Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 25:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele,+ Msiriya+ wa ku Padana-ramu, mlongo wake wa Labani, Msiriya.

  • Deuteronomo 26:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo uzikanena pamaso pa Yehova Mulungu wako kuti, ‘Bambo anga anali Msiriya+ wotsala pang’ono kufa. Anapita ku Iguputo+ ndi anthu ochepa chabe+ a m’banja lake kukakhala kumeneko monga mlendo, koma anakhaladi mtundu waukulu ndi wamphamvu kumeneko.+

  • 2 Samueli 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako Davide anamanga midzi ya asilikali+ m’dera la Asiriya a ku Damasiko ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti anali kukhoma msonkho+ kwa iye. Yehova anapitiriza kupulumutsa Davide kulikonse kumene wapita.+

  • 2 Mafumu 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano magulu achifwamba a Asiriya+ anapita kudziko la Isiraeli komwe anakagwirako kamtsikana n’kupita nako kwawo.+ Kenako kamtsikanako kanayamba kutumikira mkazi wa Namani.

  • Yesaya 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Siriya adzachokera kum’mawa+ ndipo Afilisiti adzachokera kumadzulo.+ Iwo adzadya Isiraeli ndi pakamwa potsegula.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena