Levitiko 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu asanu mwa inu adzathamangitsa adani 100, ndipo anthu 100 adzathamangitsa adani 10,000, moti mudzagonjetsa adani anu ndi lupanga.+ Deuteronomo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova adzachititsa adani ako amene adzakuukira kugonja pamaso pako.+ Pobwera kwa iwe adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pako, adzadutsa njira 7.+ Salimo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+ Salimo 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+
8 Anthu asanu mwa inu adzathamangitsa adani 100, ndipo anthu 100 adzathamangitsa adani 10,000, moti mudzagonjetsa adani anu ndi lupanga.+
7 “Yehova adzachititsa adani ako amene adzakuukira kugonja pamaso pako.+ Pobwera kwa iwe adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pako, adzadutsa njira 7.+
16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+
6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+