2 Samueli 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Yehova anatuma Natani+ kwa Davide. Natani atafika kwa Davide+ anamuuza kuti: “Panali amuna awiri amene anali kukhala mumzinda umodzi. Wina anali wolemera ndipo wina anali wosauka. 2 Samueli 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo mkazi wa ku Tekowa uja anapita kukaonana ndi mfumu, ndipo anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ kenako anadzigwetsa pansi, n’kunena kuti: “Chonde mfumu, ndipulumutseni!”+
12 Tsopano Yehova anatuma Natani+ kwa Davide. Natani atafika kwa Davide+ anamuuza kuti: “Panali amuna awiri amene anali kukhala mumzinda umodzi. Wina anali wolemera ndipo wina anali wosauka.
4 Pamenepo mkazi wa ku Tekowa uja anapita kukaonana ndi mfumu, ndipo anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ kenako anadzigwetsa pansi, n’kunena kuti: “Chonde mfumu, ndipulumutseni!”+