Miyambo 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mtima wachimwemwe umapangitsa nkhope kusangalala,+ koma chifukwa cha kupweteka kwa mtima munthu sasangalala.+ Miyambo 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mtima wa munthu ukhoza kupirira matenda,+ koma mtima wosweka ndani angaupirire?+
13 Mtima wachimwemwe umapangitsa nkhope kusangalala,+ koma chifukwa cha kupweteka kwa mtima munthu sasangalala.+