1 Mafumu 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano ine ndidzaseseratu Basa ndi nyumba yake, ndipo ndidzachititsa nyumba yake kukhala ngati nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati.+ 1 Mafumu 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye atangokhala pampando wachifumu n’kuyamba kulamulira, anapha anthu onse a m’nyumba ya Basa. Sanasiye ndi moyo munthu aliyense wokodzera khoma+ wa m’banja la Basa kapena abale ake amene akanatha kubwezera magazi ake,+ kapenanso anzake.
3 Tsopano ine ndidzaseseratu Basa ndi nyumba yake, ndipo ndidzachititsa nyumba yake kukhala ngati nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati.+
11 Iye atangokhala pampando wachifumu n’kuyamba kulamulira, anapha anthu onse a m’nyumba ya Basa. Sanasiye ndi moyo munthu aliyense wokodzera khoma+ wa m’banja la Basa kapena abale ake amene akanatha kubwezera magazi ake,+ kapenanso anzake.