2 Mbiri 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mfumu ya Isiraeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anali atakhala pabwalo* la pachipata cha Samariya. Aliyense anakhala pampando wake wachifumu, atavala zovala zachifumu.+ Aneneri onse anali pamaso pawo ndipo anali kulosera.+ Ezekieli 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, losera zokhudza aneneri a mu Isiraeli.+ Uuze amene akulosera zam’mutu mwawo+ kuti, ‘Mvetserani mawu a Yehova.+
9 Mfumu ya Isiraeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anali atakhala pabwalo* la pachipata cha Samariya. Aliyense anakhala pampando wake wachifumu, atavala zovala zachifumu.+ Aneneri onse anali pamaso pawo ndipo anali kulosera.+
2 “Iwe mwana wa munthu, losera zokhudza aneneri a mu Isiraeli.+ Uuze amene akulosera zam’mutu mwawo+ kuti, ‘Mvetserani mawu a Yehova.+