2 Mbiri 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu mfumu ya Isiraeli, kuti apite ku Ramoti-giliyadi n’kukafa?’ Choncho panali kukambirana. Uyu anali kunena zakutizakuti, uyunso n’kumanena zakutizakuti.+
19 Kenako Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu mfumu ya Isiraeli, kuti apite ku Ramoti-giliyadi n’kukafa?’ Choncho panali kukambirana. Uyu anali kunena zakutizakuti, uyunso n’kumanena zakutizakuti.+