1 Mafumu 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu, kuti apite ku Ramoti-giliyadi n’kukafa?’ Choncho uyu anayamba kunena zakutizakuti, uyunso n’kumanena zakutizakuti.+
20 Kenako Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu, kuti apite ku Ramoti-giliyadi n’kukafa?’ Choncho uyu anayamba kunena zakutizakuti, uyunso n’kumanena zakutizakuti.+