2 Mafumu 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’chaka chachisanu cha Yehoramu+ mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, pamene Yehosafati anali mfumu ya Yuda, Yehoramu+ mwana wa Yehosafati mfumu ya Yuda, anakhala mfumu. 2 Mbiri 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehoramu anayamba kulamulira ali ndi zaka 32, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8.+
16 M’chaka chachisanu cha Yehoramu+ mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, pamene Yehosafati anali mfumu ya Yuda, Yehoramu+ mwana wa Yehosafati mfumu ya Yuda, anakhala mfumu.