1 Mafumu 22:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pomalizira pake, Yehosafati anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide+ kholo lake. Kenako Yehoramu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. 2 Mbiri 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Bambo awo anawapatsa mphatso zambiri+ zasiliva, zagolide, zinthu zina zabwinozabwino, ndi mizinda ya ku Yuda+ yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Koma ufumu anaupereka kwa Yehoramu+ chifukwa ndiye anali woyamba kubadwa.+
50 Pomalizira pake, Yehosafati anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide+ kholo lake. Kenako Yehoramu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
3 Bambo awo anawapatsa mphatso zambiri+ zasiliva, zagolide, zinthu zina zabwinozabwino, ndi mizinda ya ku Yuda+ yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Koma ufumu anaupereka kwa Yehoramu+ chifukwa ndiye anali woyamba kubadwa.+