1 Mafumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Davide anagona limodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide.+ 2 Mbiri 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pomalizira pake, Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake+ mu Mzinda wa Davide. Kenako Yehoramu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
21 Pomalizira pake, Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake+ mu Mzinda wa Davide. Kenako Yehoramu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.