2 Samueli 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamene Yonatani+ ndi Ahimazi+ anali ataimirira pa Eni-rogeli,+ kapolo wamkazi anapita kumeneko ndi kuwauza zonse. Choncho iwo anachoka pakuti anafunika kukauza Mfumu Davide. Iwowa sanayese n’komwe kulowa mumzinda kuopera kuti angawazindikire.
17 Pamene Yonatani+ ndi Ahimazi+ anali ataimirira pa Eni-rogeli,+ kapolo wamkazi anapita kumeneko ndi kuwauza zonse. Choncho iwo anachoka pakuti anafunika kukauza Mfumu Davide. Iwowa sanayese n’komwe kulowa mumzinda kuopera kuti angawazindikire.