2 Samueli 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Taona, iwo ali ndi ana amuna awiri, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Choncho amuna inu mukatume amenewa kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.” 2 Samueli 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ahimazi+ mwana wa Zadoki anati: “Ndiloleni ndithamange ndikapereke uthenga kwa mfumu, chifukwa Yehova wamuweruza kuti amulanditse m’manja mwa adani ake.”+
36 Taona, iwo ali ndi ana amuna awiri, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Choncho amuna inu mukatume amenewa kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.”
19 Ndiyeno Ahimazi+ mwana wa Zadoki anati: “Ndiloleni ndithamange ndikapereke uthenga kwa mfumu, chifukwa Yehova wamuweruza kuti amulanditse m’manja mwa adani ake.”+