2 Samueli 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamene Yonatani+ ndi Ahimazi+ anali ataimirira pa Eni-rogeli,+ kapolo wamkazi anapita kumeneko ndi kuwauza zonse. Choncho iwo anachoka pakuti anafunika kukauza Mfumu Davide. Iwowa sanayese n’komwe kulowa mumzinda kuopera kuti angawazindikire. 1 Mafumu 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Akulankhula mawu amenewa, kunabwera Yonatani+ mwana wa wansembe Abiyatara. Ndipo Adoniya anati: “Lowa, uyenera kuti wabweretsa nkhani yabwino+ popeza ndiwe mwamuna wolimba mtima.”
17 Pamene Yonatani+ ndi Ahimazi+ anali ataimirira pa Eni-rogeli,+ kapolo wamkazi anapita kumeneko ndi kuwauza zonse. Choncho iwo anachoka pakuti anafunika kukauza Mfumu Davide. Iwowa sanayese n’komwe kulowa mumzinda kuopera kuti angawazindikire.
42 Akulankhula mawu amenewa, kunabwera Yonatani+ mwana wa wansembe Abiyatara. Ndipo Adoniya anati: “Lowa, uyenera kuti wabweretsa nkhani yabwino+ popeza ndiwe mwamuna wolimba mtima.”