27 Ndiyeno mlondayo anapitiriza kunena kuti: “Ndikuona kuti kathamangidwe ka munthu woyambayu kakufanana ndi kathamangidwe+ ka Ahimazi+ mwana wa Zadoki.” Atatero, mfumu inati: “Ahimazi ndi munthu wabwino,+ ndipo uthenga umene wabweretsa uyenera kukhala wabwino.”+