1 Mafumu 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Akulankhula mawu amenewa, kunabwera Yonatani+ mwana wa wansembe Abiyatara. Ndipo Adoniya anati: “Lowa, uyenera kuti wabweretsa nkhani yabwino+ popeza ndiwe mwamuna wolimba mtima.” Miyambo 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nkhani yabwino yochokera kudziko lakutali+ ili ngati madzi ozizira kwa munthu wotopa.+
42 Akulankhula mawu amenewa, kunabwera Yonatani+ mwana wa wansembe Abiyatara. Ndipo Adoniya anati: “Lowa, uyenera kuti wabweretsa nkhani yabwino+ popeza ndiwe mwamuna wolimba mtima.”