Aroma 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+ 1 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+
7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+
17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+