1 Samueli 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo Hana anati: “Pepani mbuyanga! Pali moyo wanu+ mbuyanga, ine ndine mkazi amene ndinaima ndi inu pamalo ano n’kupemphera kwa Yehova.+ 1 Mafumu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mmodzi wa akaziwo anati: “Pepani mbuyanga,+ ine ndi mayi uyu tikukhala m’nyumba imodzi. Ineyo ndinabereka mwana wamwamuna pafupi naye m’nyumbamo.
26 Pamenepo Hana anati: “Pepani mbuyanga! Pali moyo wanu+ mbuyanga, ine ndine mkazi amene ndinaima ndi inu pamalo ano n’kupemphera kwa Yehova.+
17 Mmodzi wa akaziwo anati: “Pepani mbuyanga,+ ine ndi mayi uyu tikukhala m’nyumba imodzi. Ineyo ndinabereka mwana wamwamuna pafupi naye m’nyumbamo.