1 Mafumu 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano Yehova Mulungu wanga wandipatsa mpumulo pakati pa adani anga onse ondizungulira.+ Palibe amene akulimbana nane, ndipo palibe choipa chilichonse chimene chikuchitika.+ 1 Mbiri 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona, udzabala mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wabata, ndipo ndidzam’patsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ N’chifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo,*+ ndipo m’masiku ake ndidzakhazikitsa mtendere+ ndi bata pa Isiraeli. Salimo 72:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’masiku ake, wolungama adzaphuka,+Ndipo padzakhala mtendere wochuluka kwa nthawi yonse pamene mwezi udzakhalepo.+
4 Tsopano Yehova Mulungu wanga wandipatsa mpumulo pakati pa adani anga onse ondizungulira.+ Palibe amene akulimbana nane, ndipo palibe choipa chilichonse chimene chikuchitika.+
9 Taona, udzabala mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wabata, ndipo ndidzam’patsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ N’chifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo,*+ ndipo m’masiku ake ndidzakhazikitsa mtendere+ ndi bata pa Isiraeli.
7 M’masiku ake, wolungama adzaphuka,+Ndipo padzakhala mtendere wochuluka kwa nthawi yonse pamene mwezi udzakhalepo.+