1 Mafumu 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mfumukazi ya ku Sheba+ inali kumva za Solomo, ndi zoti anatchuka chifukwa cha dzina la Yehova.+ Choncho inabwera kuti idzamuyese pomufunsa mafunso ovuta.+ 1 Mafumu 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sindinakhulupirire mawuwo mpaka pamene ndabwera n’kuona ndi maso anga, ndipo ndaona kuti ndinangouzidwa hafu chabe.+ Nzeru zanu ndi ulemerero wanu zaposa zinthu zimene ndinamva.+
10 Mfumukazi ya ku Sheba+ inali kumva za Solomo, ndi zoti anatchuka chifukwa cha dzina la Yehova.+ Choncho inabwera kuti idzamuyese pomufunsa mafunso ovuta.+
7 Sindinakhulupirire mawuwo mpaka pamene ndabwera n’kuona ndi maso anga, ndipo ndaona kuti ndinangouzidwa hafu chabe.+ Nzeru zanu ndi ulemerero wanu zaposa zinthu zimene ndinamva.+