2 Mbiri 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sindinakhulupirire+ mawuwo mpaka pamene ndabwera n’kuona ndi maso anga,+ ndipo ndaona kuti ndinangouzidwa hafu chabe ya nzeru zanu zochuluka.+ Mwaposa zinthu zimene ndinamva.+
6 Sindinakhulupirire+ mawuwo mpaka pamene ndabwera n’kuona ndi maso anga,+ ndipo ndaona kuti ndinangouzidwa hafu chabe ya nzeru zanu zochuluka.+ Mwaposa zinthu zimene ndinamva.+