Mlaliki 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ineyo ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Ine ndili ndi nzeru zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso mtima wanga wapeza nzeru zambiri ndiponso wadziwa zinthu zambiri.”+
16 Ineyo ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Ine ndili ndi nzeru zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso mtima wanga wapeza nzeru zambiri ndiponso wadziwa zinthu zambiri.”+