1 Mafumu 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iye anali wanzeru kuposa munthu wina aliyense. Anali wanzeru kuposa Etani+ mwana wa Zera, Hemani,+ Kalikoli,+ ndi Darida ana a Maholi. Ndipo anatchuka m’mitundu yonse yozungulira.+ 1 Mafumu 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo anthu ankabwera kuchokera ku mitundu yonse kudzamva nzeru za Solomo,+ ngakhalenso kuchokera kwa mafumu onse a padziko lapansi amene anamva za nzeru zake.+ 2 Mbiri 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 upatsidwa nzeru ndi luntha lodziwa zinthu.+ Ndikupatsanso katundu, chuma, ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhale,+ ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+
31 Iye anali wanzeru kuposa munthu wina aliyense. Anali wanzeru kuposa Etani+ mwana wa Zera, Hemani,+ Kalikoli,+ ndi Darida ana a Maholi. Ndipo anatchuka m’mitundu yonse yozungulira.+
34 Ndipo anthu ankabwera kuchokera ku mitundu yonse kudzamva nzeru za Solomo,+ ngakhalenso kuchokera kwa mafumu onse a padziko lapansi amene anamva za nzeru zake.+
12 upatsidwa nzeru ndi luntha lodziwa zinthu.+ Ndikupatsanso katundu, chuma, ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhale,+ ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+