2 Mbiri 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ife tidula mitengo yonse+ imene mukufunayo+ kuchokera ku Lebanoni, ndipo tiziimanga pamodzi m’maphaka oyandama n’kuitumiza kwa inu panyanja+ kukafika ku Yopa.+ Inu muzikaitengera kumeneko kupita nayo ku Yerusalemu.”
16 Ife tidula mitengo yonse+ imene mukufunayo+ kuchokera ku Lebanoni, ndipo tiziimanga pamodzi m’maphaka oyandama n’kuitumiza kwa inu panyanja+ kukafika ku Yopa.+ Inu muzikaitengera kumeneko kupita nayo ku Yerusalemu.”