Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 19:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Me-jarikoni, Rakoni, n’kukafika kumalire amene ali kutsogolo kwa Yopa.+

  • Ezara 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako anthuwo anapereka ndalama+ kwa anthu osema miyala+ ndi kwa amisiri,+ ndiponso anapereka chakudya,+ zakumwa ndi mafuta+ kwa Asidoni+ ndi kwa anthu a ku Turo,+ kuti abweretse matabwa a mkungudza kuchokera ku Lebanoni+ n’kudzawasiya m’mphepete mwa nyanja ku Yopa.+ Anachita zimenezi malinga ndi chilolezo chimene Koresi+ mfumu ya ku Perisiya anawapatsa.

  • Machitidwe 9:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Koma ku Yopa+ kunali wophunzira wina dzina lake Tabita, dzina limene polimasulira limatanthauza Dorika.* Tabita anali kuchita ntchito zabwino zambiri,+ ndi kupereka mphatso zachifundo zochuluka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena