Yoswa 19:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Me-jarikoni, Rakoni, n’kukafika kumalire amene ali kutsogolo kwa Yopa.+ 2 Mbiri 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ife tidula mitengo yonse+ imene mukufunayo+ kuchokera ku Lebanoni, ndipo tiziimanga pamodzi m’maphaka oyandama n’kuitumiza kwa inu panyanja+ kukafika ku Yopa.+ Inu muzikaitengera kumeneko kupita nayo ku Yerusalemu.”
16 Ife tidula mitengo yonse+ imene mukufunayo+ kuchokera ku Lebanoni, ndipo tiziimanga pamodzi m’maphaka oyandama n’kuitumiza kwa inu panyanja+ kukafika ku Yopa.+ Inu muzikaitengera kumeneko kupita nayo ku Yerusalemu.”