2 Mbiri 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho iye anasankhapo amuna 70,000 kuti akhale onyamula katundu,+ amuna 80,000 kuti akhale osema miyala+ kumapiri, ndi amuna 3,600 kuti akhale oyang’anira anthuwo pa ntchito yawo.+
18 Choncho iye anasankhapo amuna 70,000 kuti akhale onyamula katundu,+ amuna 80,000 kuti akhale osema miyala+ kumapiri, ndi amuna 3,600 kuti akhale oyang’anira anthuwo pa ntchito yawo.+