1 Mbiri 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Palinso antchito ambirimbiri, osema miyala,+ amisiri a miyala ndi a matabwa, ndiponso anthu onse odziwa ntchito zosiyanasiyana.+
15 Palinso antchito ambirimbiri, osema miyala,+ amisiri a miyala ndi a matabwa, ndiponso anthu onse odziwa ntchito zosiyanasiyana.+