Deuteronomo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muyenera kuphunzira zimenezi kuti muziopa+ Yehova Mulungu wanu, n’cholinga choti masiku onse a moyo wanu muzisunga mfundo zake ndi malamulo ake amene ndikukuuzani, inuyo, ana anu ndi zidzukulu zanu,+ ndiponso kuti masiku anu atalike.+ Deuteronomo 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kuti muzisunga malamulo a Yehova ndi mfundo zake+ zimene ndikukupatsani lero, kuti zinthu zikuyendereni bwino?+ Deuteronomo 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Buku limeneli azikhala nalo nthawi zonse ndipo aziliwerenga masiku onse a moyo wake,+ kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake ndi kusunga mawu onse a chilamulo ichi, kutinso azitsatira malangizo ake.+
2 Muyenera kuphunzira zimenezi kuti muziopa+ Yehova Mulungu wanu, n’cholinga choti masiku onse a moyo wanu muzisunga mfundo zake ndi malamulo ake amene ndikukuuzani, inuyo, ana anu ndi zidzukulu zanu,+ ndiponso kuti masiku anu atalike.+
13 kuti muzisunga malamulo a Yehova ndi mfundo zake+ zimene ndikukupatsani lero, kuti zinthu zikuyendereni bwino?+
19 “Buku limeneli azikhala nalo nthawi zonse ndipo aziliwerenga masiku onse a moyo wake,+ kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake ndi kusunga mawu onse a chilamulo ichi, kutinso azitsatira malangizo ake.+