1 Mafumu 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kuzungulira m’khosi mwake monse munali zokongoletsera+ zooneka ngati zipanda.+ Zinalipo 10 pa mkono uliwonse kuzungulira thanki yonseyo.+ Zokongoletsa zooneka ngati zipandazo zinalipo mizere iwiri, ndipo anaziumbira kumodzi ndi thankiyo.
24 Kuzungulira m’khosi mwake monse munali zokongoletsera+ zooneka ngati zipanda.+ Zinalipo 10 pa mkono uliwonse kuzungulira thanki yonseyo.+ Zokongoletsa zooneka ngati zipandazo zinalipo mizere iwiri, ndipo anaziumbira kumodzi ndi thankiyo.