1 Mafumu 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamatabwa a mkungudza a mkati mwa nyumbayo anajambulapo mochita kugoba zokongoletsera zooneka ngati zipanda+ ndi nkhata zamaluwa.+ Mkati monse munali matabwa a mkungudza ndipo simunkaoneka mwala uliwonse. 2 Mafumu 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho wina anapita kutchire kukathyola masamba,+ ndipo anapezako kamtengo koyanga, n’kuthyolapo mphonda zakutchire kudzaza pachovala chake. Atatero anabwera nazo n’kuziduladula. Kenako anazithira mumphika uja, koma iwo sankazidziwa bwinobwino.
18 Pamatabwa a mkungudza a mkati mwa nyumbayo anajambulapo mochita kugoba zokongoletsera zooneka ngati zipanda+ ndi nkhata zamaluwa.+ Mkati monse munali matabwa a mkungudza ndipo simunkaoneka mwala uliwonse.
39 Choncho wina anapita kutchire kukathyola masamba,+ ndipo anapezako kamtengo koyanga, n’kuthyolapo mphonda zakutchire kudzaza pachovala chake. Atatero anabwera nazo n’kuziduladula. Kenako anazithira mumphika uja, koma iwo sankazidziwa bwinobwino.