Ekisodo 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu atamva mawu odetsa nkhawa amenewa, anayamba kulira,+ ndipo palibe aliyense wa iwo anavala zodzikongoletsera. 2 Samueli 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ana aakazi a Isiraeli inu, mulirireni Sauli,Amene anakuvekani zovala zamtengo wapatali* ndi zinthu zokongoletsa,Amene anaika zokongoletsa zagolide pazovala zanu.+
4 Anthu atamva mawu odetsa nkhawa amenewa, anayamba kulira,+ ndipo palibe aliyense wa iwo anavala zodzikongoletsera.
24 Ana aakazi a Isiraeli inu, mulirireni Sauli,Amene anakuvekani zovala zamtengo wapatali* ndi zinthu zokongoletsa,Amene anaika zokongoletsa zagolide pazovala zanu.+