2 Samueli 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Seva+ anali mlembi,+ ndipo Zadoki+ ndi Abiyatara+ anali ansembe. 1 Mafumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anayamba kuchitira zinthu limodzi ndi Yowabu mwana wa Zeruya komanso wansembe Abiyatara.+ Iwowa anayamba kumuthandiza Adoniya+ monga otsatira ake.
7 Iye anayamba kuchitira zinthu limodzi ndi Yowabu mwana wa Zeruya komanso wansembe Abiyatara.+ Iwowa anayamba kumuthandiza Adoniya+ monga otsatira ake.