2 Samueli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika. 1 Mafumu 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Nkhaniyo inam’fika Yowabu,+ ndipo iye anathawira kuchihema+ cha Yehova n’kukagwira nyanga za guwa lansembe.+ Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ ngakhale kuti sanatsatire+ Abisalomu.
16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
28 Nkhaniyo inam’fika Yowabu,+ ndipo iye anathawira kuchihema+ cha Yehova n’kukagwira nyanga za guwa lansembe.+ Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ ngakhale kuti sanatsatire+ Abisalomu.