1 Mafumu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inapanganso zishango 300 zing’onozing’ono za golide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chaching’ono chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.)+ Kenako mfumuyo inaika zishangozi m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+ 2 Mbiri 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inapanganso zishango 300 zing’onozing’ono zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chaching’ono chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.)+ Kenako mfumuyo inaika zishangozi m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+ Yesaya 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndipo wina adzachotsa chophimba cha Yuda. M’tsiku limenelo, udzayang’ana kunyumba ya nkhalango yosungiramo zida zankhondo.+
17 Inapanganso zishango 300 zing’onozing’ono za golide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chaching’ono chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.)+ Kenako mfumuyo inaika zishangozi m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+
16 Inapanganso zishango 300 zing’onozing’ono zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chaching’ono chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.)+ Kenako mfumuyo inaika zishangozi m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+
8 ndipo wina adzachotsa chophimba cha Yuda. M’tsiku limenelo, udzayang’ana kunyumba ya nkhalango yosungiramo zida zankhondo.+