1 Mafumu 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamatabwa a mkungudza a mkati mwa nyumbayo anajambulapo mochita kugoba zokongoletsera zooneka ngati zipanda+ ndi nkhata zamaluwa.+ Mkati monse munali matabwa a mkungudza ndipo simunkaoneka mwala uliwonse. 1 Mafumu 6:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pazitsekopo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mitengo ya kanjedza, ndi maluwa ndipo anakuta zojambulazo ndi golide.+
18 Pamatabwa a mkungudza a mkati mwa nyumbayo anajambulapo mochita kugoba zokongoletsera zooneka ngati zipanda+ ndi nkhata zamaluwa.+ Mkati monse munali matabwa a mkungudza ndipo simunkaoneka mwala uliwonse.
35 Pazitsekopo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mitengo ya kanjedza, ndi maluwa ndipo anakuta zojambulazo ndi golide.+