Ekisodo 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Ndiyeno upange mbale zake, zikho, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Uzipange ndi golide woyenga bwino.+ Numeri 7:86 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 86 Anaperekanso zikho 12 zagolide+ zodzaza ndi zofukiza. Chikho chilichonse chinali cholemera masekeli 10, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Golide yense wa zikho zonsezi anali wolemera masekeli 120.
29 “Ndiyeno upange mbale zake, zikho, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Uzipange ndi golide woyenga bwino.+
86 Anaperekanso zikho 12 zagolide+ zodzaza ndi zofukiza. Chikho chilichonse chinali cholemera masekeli 10, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Golide yense wa zikho zonsezi anali wolemera masekeli 120.