1 Mafumu 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso, anamanga zipinda kuzungulira khoma lonse la nyumbayo, kuzungulira makoma onse akunja a chipinda chachikulu ndi chipinda chamkati.+ Anamanga zipinda zam’mbali+ zosanjikizana kuzungulira nyumba yonseyo.
5 Komanso, anamanga zipinda kuzungulira khoma lonse la nyumbayo, kuzungulira makoma onse akunja a chipinda chachikulu ndi chipinda chamkati.+ Anamanga zipinda zam’mbali+ zosanjikizana kuzungulira nyumba yonseyo.