Deuteronomo 28:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 “Yehova adzakumwazani mwa anthu a mitundu yonse kuchokera kumalekezero ena a dziko mpaka kumalekezero enanso a dziko.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina imene inuyo kapena makolo anu simunaidziwe, milungu yamtengo ndi milungu yamwala.+ Yeremiya 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ndasiya nyumba yanga.+ Ndasiya cholowa changa.+ Wokondedwa wanga ndamupereka m’manja mwa adani ake.+
64 “Yehova adzakumwazani mwa anthu a mitundu yonse kuchokera kumalekezero ena a dziko mpaka kumalekezero enanso a dziko.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina imene inuyo kapena makolo anu simunaidziwe, milungu yamtengo ndi milungu yamwala.+
7 “Ndasiya nyumba yanga.+ Ndasiya cholowa changa.+ Wokondedwa wanga ndamupereka m’manja mwa adani ake.+