Genesis 41:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pa zaka 7 zimenezo, Yosefe anasonkhanitsa chakudya chonse chimene anakolola m’dziko lonse la Iguputo, n’kuchisunga m’mizinda.+ Chakudya chonse chochokera m’minda yonse yozungulira mzinda uliwonse, anachisunga pakati pa mzindawo.+ Ekisodo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho anawaikira akulu owayang’anira pa ntchito yawo yaukapolo, kuti aziwanyamulitsa katundu mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.*
48 Pa zaka 7 zimenezo, Yosefe anasonkhanitsa chakudya chonse chimene anakolola m’dziko lonse la Iguputo, n’kuchisunga m’mizinda.+ Chakudya chonse chochokera m’minda yonse yozungulira mzinda uliwonse, anachisunga pakati pa mzindawo.+
11 Choncho anawaikira akulu owayang’anira pa ntchito yawo yaukapolo, kuti aziwanyamulitsa katundu mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.*