8 Munditumizirenso matabwa a mitengo ya mkungudza,+ mitengo ina yofanana ndi mkungudza,+ ndiponso a mitengo ya m’bawa+ kuchokera ku Lebanoni,+ popeza ndikudziwa bwino kuti antchito anu ndi akatswiri odziwa kudula mitengo ya ku Lebanoni,+ (antchito anga adzagwira ntchito pamodzi ndi antchito anu,)