Oweruza 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo ana a Isiraeli ananyamuka ndi kupita ku Beteli kukafunsira kwa Mulungu,+ kuti: “Ndani wa ife ayenera kutitsogolera kunkhondo yomenyana ndi ana a Benjamini?”+ Poyankha, Yehova anati: “Yuda akutsogolereni.”+
18 Ndipo ana a Isiraeli ananyamuka ndi kupita ku Beteli kukafunsira kwa Mulungu,+ kuti: “Ndani wa ife ayenera kutitsogolera kunkhondo yomenyana ndi ana a Benjamini?”+ Poyankha, Yehova anati: “Yuda akutsogolereni.”+