Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiyeno uike Urimu+ ndi Tumimu m’chovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamalowa kukaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula ziweruzo+ za ana a Isiraeli pamtima pake poonekera kwa Yehova nthawi zonse.

  • Numeri 27:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yoswayo aziimirira pamaso pa wansembe Eleazara, ndipo Eleazara azifunsira+ chigamulo cha Yehova m’malo mwa Yoswayo pogwiritsa ntchito maere a Urimu.+ Yoswa akalamula, ana onse a Isiraeli ndi khamu lonse azituluka naye, ndipo akalamulanso, onsewo azibwerako limodzi naye.”

  • Oweruza 20:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako ana a Isiraeli anafunsira kwa Yehova,+ chifukwa masiku amenewo likasa la pangano+ la Mulungu woona linali ku Beteli komweko.

  • Miyambo 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Uzim’kumbukira m’njira zako zonse,+ ndipo iye adzawongola njira zako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena