1 Mafumu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho anabwerera n’kutenga ng’ombe zamphongo ziwiri n’kuzipha.*+ Anatenga mitengo ya pulawo+ ya ng’ombezo n’kuphikira nyama yake. Kenako anaipereka kwa anthu kuti adye. Atatero, iye ananyamuka n’kutsatira Eliya ndipo anayamba kum’tumikira.+ Luka 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamng’ono kwambiri pa nonsenu,+ ndipo amene ali mtsogoleri akhale wotumikira.+
21 Choncho anabwerera n’kutenga ng’ombe zamphongo ziwiri n’kuzipha.*+ Anatenga mitengo ya pulawo+ ya ng’ombezo n’kuphikira nyama yake. Kenako anaipereka kwa anthu kuti adye. Atatero, iye ananyamuka n’kutsatira Eliya ndipo anayamba kum’tumikira.+
26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamng’ono kwambiri pa nonsenu,+ ndipo amene ali mtsogoleri akhale wotumikira.+